Maranatha Global

The Spirit and the bride say, “Come!” – Rev. 22:17

Chichewa (Nyanja)

The main language of Malawi, parts of Zambia, parts of Zimbabwe, and parts of Mozambique. Approximately 10 million native speakers. Also called Chewa, Chinyanja, or Nyanja.

16
Mar

malawiKUGWIRA NTCHITO MODZIPEREKA (Commitment to Service)

2 Timoteo 2:1-6

“Iwe mwana wanga, ukhale olimbika muchisomo chopezeka mwa Yesu Khristu. Ndipo zomwe wazimva kuchokera kwa ine zochitira  umboni uphunzitsenso kwa anthu ena odalirika omwenso ayenerezedwa kuphunzitsa ena. Ukhale opilira nafe m’mavuto ngati ankhondo ake a Yesu Khristu. Msilikali satanganidwanso ndi zinthu zakunja chifukwa amafuna kusangalatsa msilikali wamkulu. Chimodzimodzi ngati wina achita mpikisano, salandira mphotho mpakana atapambana molingana ndi malamulo a mpikisanowao”  Mlimi olimbika ntchito ayenera ayenera kukhala oyambilira kulandira zokolora”.

Mafanizo Atatu a Paulo

continue

Tags : , , , , , , , , , , , , , , , , , , ,
Category : Chichewa (Nyanja) | Blog
29
Sep

CHICHEWA bookVumbulutso Lodabwitsa Mu Nthawi Yathu

Maso Ndi Maso Ndi Yesu Khristu

By MaranathaGlobal.org Publications, George Chaima


Mau Ovumbulutsidwa – Teachings, lessons, and explanations in Chichewa (Nyanja)

continue


Category : Chichewa (Nyanja) | Blog
14
Sep

malawiGenesis 41:14 - Pamene iye anameta, napindula malaya ake, nalowa kwa Farao.”

Genesis 39:16 - Ndipo anaunga chofunda chake chikhale ndi iye kufikira atabwera mbuyache kwao.  Ndipo ananena kwa iye, mawu awa, Kapolo wa chihebri uja munabwera naye kuno, anabwera kudzandipunza ine.”

Genesis 37:32 - Natumiza malaya a mwinjiro, nadza kwa atate ao; ndipo anati, siawa tawatola; muzindikire tsono ngati ali malaya a mwana wanu kapena ndi ena.

Pali nyengo zitatu mu nkhani ya Yosefe m`mene anayenera kusiya chovala chake. Nthawi zonse, makamaka mu magawo awiri- anthu ena amagwiritsa nthito malaya ake ngati chinyengo kukakometsera bodza lokhudza Yosefe. China chiri chonse chomwe chinamuchitikira Yosefe chiri ndi phunziro lofanana kwa ife lero. Zikhalidwe zonse zokhudza nkhani ya Yosefe kuchitika m`magawo atatu (ngati nthawi yomwe anasiya chovala chake, kapena nthawi yomwe Mulungu anayankhula kupyolera m`maloto ndi zina zambiri) – kufotokozera za machitidwe a utatu mu cholinga cha chipulumutso.

continue

Tags : , , , , , , , ,
Category : Chichewa (Nyanja) | Blog
13
Sep

malawiGenesis 40:8 - “Ndipo iwo anati kwa iye, ife talota maloto ndipo tiribe wotimasulira.  Ndipo Yosefe anati kwa iwo, kodi mwini kumasulira si ndiye Mulungu? Mundifotokozeretu.”

Pamene Yosefe anali m`ndende ku Aigupto, anthu ena awiri anali kuyang`aniridwa ndi iye kuphatikizapo ena: woperekera chikho cha amfumu ndi wophikira mkate amfumu. Onsewa analakwira mfumu pena pake ndipo zotsatira zake ndi zoti anaponyedwa m`ndende. Usiku wina, onsewa analota maloto odabwitsa amene sanawamvetsetse ndipo anamuuza Yosefe. Maloto awo anali chizindikiro ndipo anali ndi matanthauzo awiri kapena kukwaniritsidwa kuwiri. Koyamba, loto lina liri lonse linali ndi kukwaniritsidwa nthawi yomweyo mu moyo wa munthu olotayo. Kachiwiri, loto lina liri lonse linali ndi chiyembekezo cha chinenero cholozera kwa Ambuye Yesu ndi ntchito yake ya chipulumutso.

continue

Tags : , , , , , , , ,
Category : Chichewa (Nyanja) | Blog
12
Sep

malawiGenesis 39:5-6 - ”Ndipo panali chiyambire anamuyesa Iye oyang`anira pa nyumba yake, ndi pa zache zonse, Yehova amadalitsa nyumba ya m`Aigupto chifukwa cha Yosefe: ndipo m`dalitso wa Yehova unali pa zache zonse, m`nyumba ndi m`munda.  Ndipo Iye anasiya zache zonse m`manja a Yosefe: osadziwa chomwe anali nacho, koma chakudya chomwe anadya.  Ndipo Yosefe anali wokoma thupi ndi wokongola.

Apa tikuona maphunziro awiri okhudza Ambuye Yesu. Atate wakumwamba aika zinthu zonse pansi pa ulamuliro wake, kukhulupirira mwana kumaliza cholinga cha chipulumutso. Yesu sali ngati aliyense amene tingamulambire kapena kumukhulupirira; tikuyenera kudziwa kuti ntchito yochuluka ya Ambuye ndi zolinga zonse adzisiya ntchitoyo mofuna ndi mphamvu. Iyi ndi ntchito yomwe tikuyenera kugwira nawo.

continue

Tags : , , , , , , , , , ,
Category : Chichewa (Nyanja) | Blog
11
Sep

malawi1 Samueli 16:1 - ”Ndipo Yehova ananena ndi Samueli, Iwe nkuti ulire chifukwa cha Sauli nthawi yotani popeza Ine ndinamkana kuti asakhale mfumu ya Israeli? Dzadza nyanga yako ndi mafuta, numuke, ndidzakutumiza kwa Jesse wa ku Betelehemu, pakuti ndinadzionera mfumu pakati pa ana ache.”

Samueli anakhala zaka zambiri ndi Sauli. Anatumizidwa ndi Mulungu kuti akamudzodze iye, kumulangiza iye ndi kumukweza iye monga mfumu. Ndipo amayenekera iye kumupempherera, kumulangiza iye ndi kumukhulupirira kuti ndiye adzakhala mfumu yopambana. Mu nthawi yomweyo anakatha kumuona iye kuti samayerekezera zimene zinali mwa iye, kuti m`mayesero onse amene Sauli amagwamo, kupatula mu zonse zimene Mulungu wapanga pa iye, kuphatikiza kugwiritsa ntchito Samueli monga mphumzitsi wake komanso ngati mneneri wake obweretsa mavumbulutso a Mulungu ndi malangizo.

continue

Tags : , , , , , , , , , , , ,
Category : Chichewa (Nyanja) | Blog
10
Sep

malawi1KALATA WA KWA MPINGO WA KU TIYATIRA GAWO 3

Chivumbulutso 2:20-25

“Komatu ndiri nako kutsutsana ndi iwe, kuti ulola mkazi Yezebeli, wodzitcha yekha mneneri, ndipo aphunzitsa nasocheretsa akapolo anga, kuti achite chigololo ndi udya zoperekedwa nsembe kwa mafano. Ndipo ndimpatsa nthawi kuti alape; koma safuna kulapa kusiyana nacho chigololo chake. Taona, ndimponya iye pakama, ndi iwo akuchita chigololo naye kuwalonga m`chisautso chachikulu, ngati salapa iwo ndi kuleka ntchito zake. Ndipo ndidzaononga ana ache, ndi imfa; ndipo idzazindikira mipingo kuti Ine ndine Iye amene ayesa impyso ndi mitima, ndipo ndidzaninkha kwa yense wa inu monga mwa ntchtio zanu. Koma ndinena kwa inu, kwa otsala aku Tiyatira, onse omwe alibe chiphunzitso ichi sanazindikira zakuya za satana, momga anena sindikusanjikizani katundu wina. Koma chimene muli nacho gwirani kufikira ndikadza…”

continue

Tags : , , , , , , , , ,
Category : Chichewa (Nyanja) | Blog
9
Sep

malawiABRAHAMU APULUMUTSA LOTI

Abrahamu anapulumutsa Loti katatu konse. Poyambilira anamuchotsa mu dziko la Harani ndi kupita naye ku dziko la lonjezano. Kachiwiri anamupulumutsa pamene anatengedwa mu ukapolo ndi mafumu akumwera. Kachitatu anamupempherera pamene Sodomu ndi Gomola anali pafupi kuonongeka. Kupyolera mu njira zitatu zimenezi, tikuona kuchita utatu mu chipulumutso chathu.

continue

Tags : , , , , , , , , ,
Category : Chichewa (Nyanja) | Blog
9
Sep

malawi1MBIYA M`MANJA MWA OUMBA:  (Clay pot in a potter’s hands)

Yeremiya 18:6

“Monga ngati m`manja mwa oumba mbiya ndiye simuli m`manja mwanga inu nyumba ya Israeli?”

Bukhu lothandizira, Masalmo 139:16-17 ” Ndisanaumbidwe ine, maso anu anandipanga, ziwalo zanga zonse zinalembedwa m`bukhu mwanu, masiku akuti zilembedwe, panalibe chimodzi cha izo. Potero, Mulungu, ndidziyesa zolingalira zanu za mtengo wache ndithu! Mawerengedwe ake ndi ambiri:

continue

Tags : , , , , , , , ,
Category : Chichewa (Nyanja) | Blog
9
Sep

oliveoil21-150x1501KUDZODZA KWA ARONI NDI ANA AKE - Levitiko 8:22-24

“Ndipo anabwera nayo nkhosa yamphongo yinayo, ndiyo mphongo yakudzadza m`manja; ndipo Aroni ndi ana ache amuna anaika manja awo pa mutu pa mphongoyo; ndi Mose anatengako mwazi wache wakupaka pa ndewere ya khutu la kudzanja lamanja la Aroni, ndi pa chala chachikuru cha phanzi lake la ku dzanja la manja.”

Gawo limeneli likufotokoza kulumikizana kwa Aroni ndi ana ache amuna, mu nthawi yoyamba ya chipangano cha kale chomwe Mulungu amalamulira amuna mu utumiki. Zinali ndi maphunziro abwino kwa ife okhulupirira lero. Chipangano chatsopano chikutiphunzitsa ife kuti okhulupirira tsopano ndi ansembe-onse okhulupirira ndi mbali imodzi ya unsembe wa okhulupirira. “Ali ngatinso mwala wa moyo, akumangira nyumba ya uzimu kukhala malo oyera, operekera nsembe za uzimu, pfuko loyera, anthu a Mulungu. 1Petro 2:9, “kukhla mtumiki wa Yesu kwa amitundu ndi ntchito yoperekera uthenga wabwino kwa iwo, kuti amitundu akhale nsembe yovomerezeka kwa Mulungu, yoperekedwa ndi Mzimu Woyera.” Aroma 15:16.

continue

Tags : , , , , , , , , , ,
Category : Chichewa (Nyanja) | Blog